2 Mbiri 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Ahazi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mumzinda wa Yerusalemu. Iye sanaikidwe mʼmanda a mafumu a Isiraeli.+ Ndiyeno Hezekiya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
27 Kenako Ahazi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mumzinda wa Yerusalemu. Iye sanaikidwe mʼmanda a mafumu a Isiraeli.+ Ndiyeno Hezekiya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.