2 Mbiri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Muchotse mʼmalo oyera chinthu chilichonse chodetsedwa.+
5 Ndiyeno anawauza kuti: “Tamverani Alevi inu. Dziyeretseni+ ndipo muyeretsenso nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo anu. Muchotse mʼmalo oyera chinthu chilichonse chodetsedwa.+