2 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa makolo athu akhala akuchita zosakhulupirika ndiponso zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya komanso anasiya chihema chopatulika cha Yehova nʼkumulozetsa nkhongo.+
6 Chifukwa makolo athu akhala akuchita zosakhulupirika ndiponso zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wathu.+ Iwo anamusiya komanso anasiya chihema chopatulika cha Yehova nʼkumulozetsa nkhongo.+