2 Mbiri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatseka zitseko zapakhonde+ ndiponso anazimitsa nyale.+ Komanso anasiya kupereka nsembe zofukiza+ ndi nsembe zopsereza+ kwa Mulungu wa Isiraeli mʼmalo oyera.
7 Anatseka zitseko zapakhonde+ ndiponso anazimitsa nyale.+ Komanso anasiya kupereka nsembe zofukiza+ ndi nsembe zopsereza+ kwa Mulungu wa Isiraeli mʼmalo oyera.