2 Mbiri 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa chifukwa chimenechi, makolo athu anaphedwa ndi lupanga+ ndipo ana athu aamuna ndi aakazi ndiponso akazi athu anatengedwa kupita ku ukapolo.+
9 Pa chifukwa chimenechi, makolo athu anaphedwa ndi lupanga+ ndipo ana athu aamuna ndi aakazi ndiponso akazi athu anatengedwa kupita ku ukapolo.+