2 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anasonkhanitsa abale awo nʼkudziyeretsa. Ndiyeno anabwera kudzayeretsa nyumba ya Yehova mogwirizana ndi lamulo la mfumu potsatira mawu a Yehova.+
15 Kenako anasonkhanitsa abale awo nʼkudziyeretsa. Ndiyeno anabwera kudzayeretsa nyumba ya Yehova mogwirizana ndi lamulo la mfumu potsatira mawu a Yehova.+