2 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo anapha ngʼombezo+ ndipo ansembe anatenga magazi ake nʼkuwaza paguwa lansembe.+ Kenako anapha nkhosa zamphongo zija nʼkuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja nʼkuwaza magazi ake paguwa lansembe.
22 Iwo anapha ngʼombezo+ ndipo ansembe anatenga magazi ake nʼkuwaza paguwa lansembe.+ Kenako anapha nkhosa zamphongo zija nʼkuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja nʼkuwaza magazi ake paguwa lansembe.