2 Mbiri 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nsembe zopsereza zimene gulu la anthuwo linabweretsa zinalipo ngʼombe 70, nkhosa zamphongo 100 ndi ana a nkhosa amphongo 200. Zonsezi anazipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza.+
32 Nsembe zopsereza zimene gulu la anthuwo linabweretsa zinalipo ngʼombe 70, nkhosa zamphongo 100 ndi ana a nkhosa amphongo 200. Zonsezi anazipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza.+