2 Mbiri 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Komanso, panali nsembe zopsereza zambiri+ ndiponso mafuta ambiri a nsembe zamgwirizano.+ Nazonso nsembe zachakumwa zimene zinaperekedwa limodzi ndi nsembe zopserezazo zinali zambiri.+ Choncho utumiki wapanyumba ya Yehova unayambiranso kuchitika.
35 Komanso, panali nsembe zopsereza zambiri+ ndiponso mafuta ambiri a nsembe zamgwirizano.+ Nazonso nsembe zachakumwa zimene zinaperekedwa limodzi ndi nsembe zopserezazo zinali zambiri.+ Choncho utumiki wapanyumba ya Yehova unayambiranso kuchitika.