2 Mbiri 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho asilikali othamangawo anapita mʼmizinda yonse mʼdera la Efuraimu ndi Manase+ mpaka ku Zebuloni. Koma anthuwo ankangowanyoza ndiponso kuwaseka.+
10 Choncho asilikali othamangawo anapita mʼmizinda yonse mʼdera la Efuraimu ndi Manase+ mpaka ku Zebuloni. Koma anthuwo ankangowanyoza ndiponso kuwaseka.+