-
2 Mbiri 30:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Komanso dzanja la Mulungu woona linathandiza anthu a ku Yuda kukhala ogwirizana, kuti amvere zimene mfumu ndi akalonga anawalamula motsatira mawu a Yehova.
-