2 Mbiri 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako iwo anakachotsa maguwa ansembe amene anali mu Yerusalemu.+ Anachotsanso maguwa onse a nsembe zofukiza+ nʼkukawataya kuchigwa cha Kidironi.
14 Kenako iwo anakachotsa maguwa ansembe amene anali mu Yerusalemu.+ Anachotsanso maguwa onse a nsembe zofukiza+ nʼkukawataya kuchigwa cha Kidironi.