2 Mbiri 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anaimirira mʼmalo mwawo mogwirizana ndi Chilamulo cha Mose munthu wa Mulungu woona. Kenako ansembe anawaza paguwa lansembe magazi+ amene analandira kwa Alevi.
16 Iwo anaimirira mʼmalo mwawo mogwirizana ndi Chilamulo cha Mose munthu wa Mulungu woona. Kenako ansembe anawaza paguwa lansembe magazi+ amene analandira kwa Alevi.