2 Mbiri 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pagululo panali anthu ambiri amene sanadziyeretse. Choncho Alevi ndi amene ankapha nyama za Pasika za anthu onse amene sanali oyera,+ kuti awayeretse kwa Yehova.
17 Pagululo panali anthu ambiri amene sanadziyeretse. Choncho Alevi ndi amene ankapha nyama za Pasika za anthu onse amene sanali oyera,+ kuti awayeretse kwa Yehova.