18 Anthu ambiri makamaka ochokera ku Efuraimu, ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni sanadziyeretse koma anadyabe Pasikayo, zomwe zinali zosagwirizana ndi zimene zinalembedwa. Ndiyeno Hezekiya anawapempherera kuti: “Inu Yehova, ndinu wabwino,+ musakwiyire