2 Mbiri 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 aliyense amene wakonza mtima wake kuti afunefune inu Mulungu woona+ Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi malamulo okhudza kudziyeretsa.”+
19 aliyense amene wakonza mtima wake kuti afunefune inu Mulungu woona+ Yehova, Mulungu wa makolo ake, ngakhale kuti sanadziyeretse mogwirizana ndi malamulo okhudza kudziyeretsa.”+