2 Mbiri 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Hezekiya mfumu ya Yuda anapereka ku mpingowo ngʼombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 7,000. Akalonganso anapereka ku mpingowo ngʼombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 10,000+ ndipo ansembe ambiri ankadziyeretsa.+
24 Hezekiya mfumu ya Yuda anapereka ku mpingowo ngʼombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 7,000. Akalonganso anapereka ku mpingowo ngʼombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 10,000+ ndipo ansembe ambiri ankadziyeretsa.+