2 Mbiri 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Gulu lonse la Ayuda, ansembe, Alevi, gulu lonse la anthu amene anachokera ku Isiraeli+ komanso alendo+ amene anachokera mʼdziko la Isiraeli ndiponso amene ankakhala mʼdziko la Yuda, anapitiriza kusangalala.
25 Gulu lonse la Ayuda, ansembe, Alevi, gulu lonse la anthu amene anachokera ku Isiraeli+ komanso alendo+ amene anachokera mʼdziko la Isiraeli ndiponso amene ankakhala mʼdziko la Yuda, anapitiriza kusangalala.