2 Mbiri 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthuwo anapitiriza kubweretsa zopereka mokhulupirika, chakhumi+ ndi zinthu zopatulika. Konaniya Mlevi anaikidwa kuti akhale woyangʼanira zinthu zonsezi ndipo Simeyi mchimwene wake anali wachiwiri wake.
12 Anthuwo anapitiriza kubweretsa zopereka mokhulupirika, chakhumi+ ndi zinthu zopatulika. Konaniya Mlevi anaikidwa kuti akhale woyangʼanira zinthu zonsezi ndipo Simeyi mchimwene wake anali wachiwiri wake.