-
2 Mbiri 31:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Yehiela, Azaziya, Nahati, Asaheli, Yerimoti, Yozabadi, Elieli, Isimakiya, Mahati ndi Benaya ankathandiza Konaniya ndi Simeyi mchimwene wake motsatira lamulo la Mfumu Hezekiya. Azariya anali mtsogoleri wa nyumba ya Mulungu woona.
-