2 Mbiri 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kore, mwana wa Imuna mlonda wa fuko la Levi wapageti lakumʼmawa,+ ankayangʼanira zopereka zaufulu+ za Mulungu woona ndiponso ankagawa zinthu zoperekedwa kwa Yehova+ ndi zinthu zopatulika koposa.+
14 Kore, mwana wa Imuna mlonda wa fuko la Levi wapageti lakumʼmawa,+ ankayangʼanira zopereka zaufulu+ za Mulungu woona ndiponso ankagawa zinthu zoperekedwa kwa Yehova+ ndi zinthu zopatulika koposa.+