-
2 Mbiri 31:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Hezekiya anachita zimenezi ku Yuda konse ndipo anapitiriza kuchita zabwino, zoyenera komanso zokhulupirika pamaso pa Yehova Mulungu wake.
-