2 Mbiri 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anagwira ndi mtima wake wonse ntchito iliyonse imene anaiyamba pofunafuna Mulungu wake, kaya ndi yokhudza utumiki wapanyumba ya Mulungu woona+ kapena Chilamulo, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.
21 Anagwira ndi mtima wake wonse ntchito iliyonse imene anaiyamba pofunafuna Mulungu wake, kaya ndi yokhudza utumiki wapanyumba ya Mulungu woona+ kapena Chilamulo, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.