-
2 Mbiri 32:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Anthu ambiri anasonkhana ndipo anatseka akasupe onse ndiponso mtsinje umene unkadutsa kumeneko. Iwo anati: “Sitikufuna kuti mafumu a Asuri akabwera adzakhale ndi madzi ambiri.”
-