2 Mbiri 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu. Musachite mantha kapena kuopa mfumu ya Asuri+ ndi gulu lalikulu limene ali nalo, chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.+
7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu. Musachite mantha kapena kuopa mfumu ya Asuri+ ndi gulu lalikulu limene ali nalo, chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.+