2 Mbiri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye akudalira mphamvu za anthu, koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Anthuwo analimbikitsidwa kwambiri ndi mawu amene Hezekiya mfumu ya Yuda inanenawa.+
8 Iye akudalira mphamvu za anthu, koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Anthuwo analimbikitsidwa kwambiri ndi mawu amene Hezekiya mfumu ya Yuda inanenawa.+