2 Mbiri 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Senakeribu mfumu ya Asuri ali ku Lakisi+ pamodzi ndi asilikali ake onse, anatuma anthu ku Yerusalemu kwa Hezekiya mfumu ya Yuda ndi kwa anthu onse a ku Yudeya omwe anali ku Yerusalemu.+ Anawatuma kukanena kuti:
9 Kenako Senakeribu mfumu ya Asuri ali ku Lakisi+ pamodzi ndi asilikali ake onse, anatuma anthu ku Yerusalemu kwa Hezekiya mfumu ya Yuda ndi kwa anthu onse a ku Yudeya omwe anali ku Yerusalemu.+ Anawatuma kukanena kuti: