2 Mbiri 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Senakeribu mfumu ya Asuri yanena kuti, ‘Kodi mukudalira chiyani kuti muzingokhalabe mu Yerusalemu, mzindawu utazunguliridwa?+
10 “Senakeribu mfumu ya Asuri yanena kuti, ‘Kodi mukudalira chiyani kuti muzingokhalabe mu Yerusalemu, mzindawu utazunguliridwa?+