2 Mbiri 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi si Hezekiya yemweyo amene anachotsa malo okwezeka+ a Mulungu wanu ndi maguwa ake ansembe+ kenako nʼkuuza anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti: “Muziwerama pamaso pa guwa lansembe limodzi lokha ndipo nsembe zanu muzipereka pamenepo”?+
12 Kodi si Hezekiya yemweyo amene anachotsa malo okwezeka+ a Mulungu wanu ndi maguwa ake ansembe+ kenako nʼkuuza anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti: “Muziwerama pamaso pa guwa lansembe limodzi lokha ndipo nsembe zanu muzipereka pamenepo”?+