2 Mbiri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi simukudziwa zimene ineyo ndi makolo anga akale tinachita kwa anthu onse a mayiko ena?+ Kodi milungu ya anthu a mitundu inayo inatha kupulumutsa mayiko awo mʼmanja mwanga?+
13 Kodi simukudziwa zimene ineyo ndi makolo anga akale tinachita kwa anthu onse a mayiko ena?+ Kodi milungu ya anthu a mitundu inayo inatha kupulumutsa mayiko awo mʼmanja mwanga?+