17 lye analembanso makalata+ onyoza Yehova Mulungu wa Isiraeli+ komanso omunenera zachipongwe kuti: “Mofanana ndi milungu ya anthu amʼmayiko ena, imene sinapulumutse anthu ake mʼmanja mwanga,+ Mulungu wa Hezekiya sapulumutsa anthu ake mʼmanja mwanga.”