2 Mbiri 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anapitiriza kulankhula mokuwa mʼchilankhulo cha Ayuda, kwa anthu a ku Yerusalemu amene anali pamwamba pa mpanda, kuti awaopseze komanso kuwachititsa mantha nʼcholinga choti alande mzindawo.+
18 Iwo anapitiriza kulankhula mokuwa mʼchilankhulo cha Ayuda, kwa anthu a ku Yerusalemu amene anali pamwamba pa mpanda, kuti awaopseze komanso kuwachititsa mantha nʼcholinga choti alande mzindawo.+