2 Mbiri 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Mfumu Hezekiya ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi, ankapempherera nkhani imeneyi ndiponso kufuulira Mulungu kumwamba kuti awathandize.+
20 Koma Mfumu Hezekiya ndi mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi, ankapempherera nkhani imeneyi ndiponso kufuulira Mulungu kumwamba kuti awathandize.+