2 Mbiri 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:23 Yesaya 1, tsa. 396
23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse.