2 Mbiri 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mʼmasiku amenewo, Hezekiya anadwala mpaka kutsala pangʼono kufa. Iye anapemphera kwa Yehova+ ndipo anamuyankha komanso anamupatsa chizindikiro.+
24 Mʼmasiku amenewo, Hezekiya anadwala mpaka kutsala pangʼono kufa. Iye anapemphera kwa Yehova+ ndipo anamuyankha komanso anamupatsa chizindikiro.+