-
2 Mbiri 32:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Koma Hezekiya sanasonyeze kuyamikira zabwino zimene anamuchitira, moti mtima wake unayamba kudzikuza ndipo zimenezi zinachititsa kuti Mulungu amukwiyire iyeyo, Yuda ndiponso Yerusalemu.
-