2 Mbiri 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Hezekiya anakhala ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero.+ Anamanga nyumba zake zosungiramo+ siliva, golide, miyala yamtengo wapatali, mafuta a basamu, zishango ndiponso zinthu zonse zabwino kwambiri. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:27 Yesaya 1, tsa. 396
27 Hezekiya anakhala ndi chuma chambiri ndiponso ulemerero.+ Anamanga nyumba zake zosungiramo+ siliva, golide, miyala yamtengo wapatali, mafuta a basamu, zishango ndiponso zinthu zonse zabwino kwambiri.