-
2 Mbiri 32:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Analinso ndi mizinda ndiponso ziweto zosiyanasiyana monga nkhosa ndi ngʼombe zambiri, chifukwa Mulungu anamʼpatsa katundu wambiri.
-