2 Mbiri 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hezekiya ndi amene anatseka kasupe wakumtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsira kumunsi, chakumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya ankagwira inkamuyendera bwino. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:30 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 20-21 Nsanja ya Olonda,6/15/1997, ptsa. 9-108/15/1996, ptsa. 5-6
30 Hezekiya ndi amene anatseka kasupe wakumtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsira kumunsi, chakumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya ankagwira inkamuyendera bwino.