2 Mbiri 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma akalonga a ku Babulo atatumiza anthu kuti akamufunse za chizindikiro+ chimene chinachitika mʼdzikolo,+ Mulungu woona anamusiya kuti amuyese+ nʼcholinga choti adziwe zonse zimene zinali mumtima mwake.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:31 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2017, tsa. 26
31 Koma akalonga a ku Babulo atatumiza anthu kuti akamufunse za chizindikiro+ chimene chinachitika mʼdzikolo,+ Mulungu woona anamusiya kuti amuyese+ nʼcholinga choti adziwe zonse zimene zinali mumtima mwake.+