2 Mbiri 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova ndipo ankatsatira zinthu zonyansa zomwe ankachita anthu a mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa Aisiraeli.+
2 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova ndipo ankatsatira zinthu zonyansa zomwe ankachita anthu a mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa Aisiraeli.+