2 Mbiri 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anagwetsa.+ Anamanga maguwa ansembe a Abaala komanso mizati yopatulika,* ndipo ankagwadira gulu lonse la zinthu zakumwamba ndiponso kuzitumikira.+
3 Iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anagwetsa.+ Anamanga maguwa ansembe a Abaala komanso mizati yopatulika,* ndipo ankagwadira gulu lonse la zinthu zakumwamba ndiponso kuzitumikira.+