2 Mbiri 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanganso maguwa ansembe mʼnyumba ya Yehova,+ imene Yehova ananena kuti: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+
4 Anamanganso maguwa ansembe mʼnyumba ya Yehova,+ imene Yehova ananena kuti: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+