2 Mbiri 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anamanga maguwa ansembe a gulu lonse la zinthu zakumwamba mʼmabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+