-
2 Mbiri 33:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Sindidzachotsanso mapazi a Aisiraeli mʼdziko limene ndinapereka kwa makolo awo, ngati atayesetsa kutsatira zonse zimene ndinawalamula zomwe ndi Chilamulo chonse, malangizo onse ndi ziweruzo zonse zimene ndinawapatsa kudzera mwa Mose.”
-