2 Mbiri 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Manase anapitiriza kusocheretsa Yuda ndi anthu a ku Yerusalemu ndipo anawachititsa kuti azichita zinthu zoipa kuposa zimene ankachita anthu a mitundu yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa Aisiraeli.+
9 Manase anapitiriza kusocheretsa Yuda ndi anthu a ku Yerusalemu ndipo anawachititsa kuti azichita zinthu zoipa kuposa zimene ankachita anthu a mitundu yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa Aisiraeli.+