2 Mbiri 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Manase ndiponso anthu ake, koma iwo sanamvere.+