2 Mbiri 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova anawabweretsera atsogoleri a asilikali a mfumu ya Asuri ndipo anagwira Manase ndi ngowe.* Atatero anamʼmanga ndi matcheni awiri akopa* nʼkupita naye ku Babulo. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:11 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 28
11 Choncho Yehova anawabweretsera atsogoleri a asilikali a mfumu ya Asuri ndipo anagwira Manase ndi ngowe.* Atatero anamʼmanga ndi matcheni awiri akopa* nʼkupita naye ku Babulo.