2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva pemphero lake lochonderera ndiponso lopempha chifundo. Kenako anamʼbwezera ku Yerusalemu ndipo anakhalanso mfumu.+ Zitatero, Manase anadziwa kuti Yehova ndi Mulungu woona.+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva pemphero lake lochonderera ndiponso lopempha chifundo. Kenako anamʼbwezera ku Yerusalemu ndipo anakhalanso mfumu.+ Zitatero, Manase anadziwa kuti Yehova ndi Mulungu woona.+