2 Mbiri 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anachotsa milungu yachilendo, fano limene linali mʼnyumba ya Yehova+ ndi maguwa onse ansembe amene anamanga mʼphiri la nyumba ya Yehova+ ndi mu Yerusalemu. Atatero anakataya zinthu zimenezi kunja kwa mzindawo.
15 Kenako anachotsa milungu yachilendo, fano limene linali mʼnyumba ya Yehova+ ndi maguwa onse ansembe amene anamanga mʼphiri la nyumba ya Yehova+ ndi mu Yerusalemu. Atatero anakataya zinthu zimenezi kunja kwa mzindawo.